2 Mbiri 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha+ kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo. Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha, kenako iwo anayamba kumenya nawo nkhondo.+
29 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha+ kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo. Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha, kenako iwo anayamba kumenya nawo nkhondo.+