1 Mafumu 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo.+ Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha+ n’kuyamba kumenya nawo nkhondo.+
30 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo.+ Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha+ n’kuyamba kumenya nawo nkhondo.+