2 Mbiri 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yosiya anapitabe kukakumana naye+ ndipo anadzisintha+ kuti amenyane naye. Iye sanamvere mawu a Neko+ ochokera pakamwa pa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye m’chigwa cha Megido.+ Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+
22 Koma Yosiya anapitabe kukakumana naye+ ndipo anadzisintha+ kuti amenyane naye. Iye sanamvere mawu a Neko+ ochokera pakamwa pa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye m’chigwa cha Megido.+