1 Mafumu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anali atauza Ahiya kuti: “Kukubwera mkazi wa Yerobowamu kudzakufunsa za mwana wake, chifukwa mwanayo akudwala. Umuuze zakutizakuti. Zomwe zichitike n’zakuti, akangofika adzisintha kuti asadziwike.”+ 1 Mafumu 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako, mneneriyo anakaima m’mphepete mwa msewu n’kumakadikirira mfumu ija, atadzimanga kansalu kumaso kuti asadziwike.+
5 Yehova anali atauza Ahiya kuti: “Kukubwera mkazi wa Yerobowamu kudzakufunsa za mwana wake, chifukwa mwanayo akudwala. Umuuze zakutizakuti. Zomwe zichitike n’zakuti, akangofika adzisintha kuti asadziwike.”+
38 Kenako, mneneriyo anakaima m’mphepete mwa msewu n’kumakadikirira mfumu ija, atadzimanga kansalu kumaso kuti asadziwike.+