1 Samueli 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako anapereka chakudyacho kwa Sauli ndi atumiki ake ndipo iwo anadya. Atamaliza ananyamuka usiku womwewo.+
25 Kenako anapereka chakudyacho kwa Sauli ndi atumiki ake ndipo iwo anadya. Atamaliza ananyamuka usiku womwewo.+