1 Samueli 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Sauli anadzisintha+ ndi kuvala zovala zina. Atatero, iyeyo ndi amuna ena awiri anapita kwa mkaziyo ndipo anafikako usiku.+ Ndiyeno Sauliyo anati: “Ndiloserere zam’tsogolo+ mwa kulankhula ndi mizimu ndipo undiutsire munthu amene ndikuuze.”
8 Choncho Sauli anadzisintha+ ndi kuvala zovala zina. Atatero, iyeyo ndi amuna ena awiri anapita kwa mkaziyo ndipo anafikako usiku.+ Ndiyeno Sauliyo anati: “Ndiloserere zam’tsogolo+ mwa kulankhula ndi mizimu ndipo undiutsire munthu amene ndikuuze.”