1 Mafumu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka, udzisinthe+ kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu ndipo upite ku Silo. Kumeneko n’kumene kuli mneneri Ahiya.+ Ameneyo ndiye anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+ 1 Mafumu 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo.+ Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha+ n’kuyamba kumenya nawo nkhondo.+
2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka, udzisinthe+ kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu ndipo upite ku Silo. Kumeneko n’kumene kuli mneneri Ahiya.+ Ameneyo ndiye anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+
30 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo.+ Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha+ n’kuyamba kumenya nawo nkhondo.+