-
Oweruza 9:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno Mulungu analola kuti pakhale chidani pakati pa Abimeleki ndi atsogoleri a ku Sekemu, moti atsogoleriwo anayamba kuchitira Abimeleki zachinyengo.
-