Oweruza 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mulungu analola kuti pakhale kusamvana+ pakati pa Abimeleki ndi nzika za Sekemu, moti nzika za Sekemu zinayamba kuchitira Abimeleki zachinyengo.+
23 Ndiyeno Mulungu analola kuti pakhale kusamvana+ pakati pa Abimeleki ndi nzika za Sekemu, moti nzika za Sekemu zinayamba kuchitira Abimeleki zachinyengo.+