Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+ Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+ Hoseya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+
48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+ Hoseya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+
3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+