Mika 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mawu a Yehova akumveka mumzinda.+ Munthu wanzeru zopindulitsa adzaopa dzina lanu.+ Anthu inu, mverani mawu a ndodo ndi a amene anaisankha.+
9 Mawu a Yehova akumveka mumzinda.+ Munthu wanzeru zopindulitsa adzaopa dzina lanu.+ Anthu inu, mverani mawu a ndodo ndi a amene anaisankha.+