Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu ochokera m’mitundu yosiyanasiyana adzabwera n’kunena kuti: “Bwerani+ anthu inu. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova. Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo. Iye akatiphunzitsa njira zake, ndipo ife tidzayenda m’njira zakezo.”+ Pakuti mu Ziyoni mudzatuluka malamulo ndipo mawu a Yehova adzatuluka mu Yerusalemu.+

  • Yesaya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu amuna a m’nyumba ya Yakobo, bwerani tidzayende m’kuwala kwa Yehova.+

  • Yesaya 30:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Makutu ako adzamva mawu kumbuyo kwako, akuti: “Njira ndi iyi.+ Yendani mmenemu anthu inu.” Yendani m’njira imeneyi kuti musasochere n’kulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena