Yeremiya 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika. Malaki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+
15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika.
4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+