1 Mafumu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. ‘Popeza watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+
20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. ‘Popeza watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+