-
Yeremiya 44:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Mawu awa akukhudza amuna inu ndi akazi anu.+ Akazi inu mumalankhula ndi pakamwa panu (ndipo anthu nonsenu mwakwaniritsa zonena zanu ndi manja anu) kuti: “Ife tidzakwaniritsa malonjezo athu+ akuti ‘tidzapereka nsembe zautsi kwa ‘mfumukazi yakumwamba’+ ndi kuti tidzapereka nsembe yachakumwa kwa iye.”+ Akazi inu mudzachitadi zimene mwalonjeza ndipo mudzakwaniritsadi malonjezo anu.’
-