1 Mafumu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ 1 Mafumu 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.
28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.