1 Mafumu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ 2 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Tsopano anthu inu mukuganiza zolimbana ndi ufumu wa Yehova umene uli m’manja mwa ana a Davide,+ popeza ndinu khamu lalikulu+ ndipo muli ndi ana a ng’ombe agolide amene Yerobowamu anakupangirani kuti akhale milungu yanu.+
28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
8 “Tsopano anthu inu mukuganiza zolimbana ndi ufumu wa Yehova umene uli m’manja mwa ana a Davide,+ popeza ndinu khamu lalikulu+ ndipo muli ndi ana a ng’ombe agolide amene Yerobowamu anakupangirani kuti akhale milungu yanu.+