Ekisodo 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Musadzipangire milungu ya mafano opangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Levitiko 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.