1 Mafumu 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Komanso, ngati kuti kuyenda m’machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati inali nkhani yaing’ono,+ Ahabu anakwatira+ Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kukatumikira Baala+ ndi kum’gwadira. 1 Mafumu 22:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Ahaziya anapitiriza kutumikira Baala+ ndi kum’gwadira, ndipo anapitiriza kukwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, malinga ndi zonse zimene bambo ake anachita. 2 Mafumu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Yehu anatumiza uthenga mu Isiraeli+ yense, moti olambira onse a Baala+ anabwera. Palibe ndi mmodzi yemwe amene sanabwere. Iwo analowa m’kachisi wa Baala ndipo kachisiyo anadzaza kuchokera kutsogolo mpaka kumbuyo.
31 Komanso, ngati kuti kuyenda m’machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati inali nkhani yaing’ono,+ Ahabu anakwatira+ Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kukatumikira Baala+ ndi kum’gwadira.
53 Ahaziya anapitiriza kutumikira Baala+ ndi kum’gwadira, ndipo anapitiriza kukwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, malinga ndi zonse zimene bambo ake anachita.
21 Kenako Yehu anatumiza uthenga mu Isiraeli+ yense, moti olambira onse a Baala+ anabwera. Palibe ndi mmodzi yemwe amene sanabwere. Iwo analowa m’kachisi wa Baala ndipo kachisiyo anadzaza kuchokera kutsogolo mpaka kumbuyo.