Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakhale ndi milungu ina iliyonse+ kupatulapo ine.* Ekisodo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+
14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+