-
Oweruza 10:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zitatero, ana a Isiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndipo anayamba kutumikira Abaala,+ zifaniziro za Asitoreti,+ milungu ya ku Siriya,+ milungu ya ku Sidoni,+ milungu ya ku Mowabu,+ milungu ya ana a Amoni+ ndi milungu ya Afilisiti.+ Motero iwo anasiya Yehova ndipo sanam’tumikire.+
-
-
2 Mafumu 10:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Tsopano itanani aneneri+ onse a Baala, olambira ake onse,+ ndi ansembe ake+ onse kuti abwere kwa ine. Pasapezeke aliyense wotsala chifukwa ndakonza nsembe yaikulu yoti ndipereke kwa Baala. Aliyense amene palibe sakhala ndi moyo.” Koma Yehu anawapusitsa+ n’cholinga choti awononge anthu olambira Baala.
-