Miyambo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+ Mlaliki 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti munthu+ nayenso sadziwa nthawi yake.+ Monga nsomba zimene zagwidwa mu ukonde wakupha,+ ndi mbalame zimene zakodwa mumsampha,+ ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka,+ nthawiyo ikawafikira mwadzidzidzi.+
6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
12 Pakuti munthu+ nayenso sadziwa nthawi yake.+ Monga nsomba zimene zagwidwa mu ukonde wakupha,+ ndi mbalame zimene zakodwa mumsampha,+ ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka,+ nthawiyo ikawafikira mwadzidzidzi.+