Luka 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Koma samalani kuti mitima yanu isalemedwe ndi kudya kwambiri, kumwa kwambiri,+ ndi nkhawa+ za moyo, kuti tsikulo lingadzakufikireni modzidzimutsa+
34 “Koma samalani kuti mitima yanu isalemedwe ndi kudya kwambiri, kumwa kwambiri,+ ndi nkhawa+ za moyo, kuti tsikulo lingadzakufikireni modzidzimutsa+