Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Yesaya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko lina chifukwa chosadziwa zinthu.+ Anthu awo olemekezeka adzakhala amuna anjala+ ndipo khamu lawo lidzakhala louma kukhosi ndi ludzu.+ Aroma 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje.
4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
13 Chotero anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko lina chifukwa chosadziwa zinthu.+ Anthu awo olemekezeka adzakhala amuna anjala+ ndipo khamu lawo lidzakhala louma kukhosi ndi ludzu.+
13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje.