2 Akorinto 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+ Tito 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwe pewa mafunso opusa,+ kukumba mibadwo ya makolo,+ mikangano+ ndi kulimbana pa za Chilamulo,+ chifukwa zimenezi n’zosapindulitsa ndiponso n’zachabechabe.
20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+
9 Koma iwe pewa mafunso opusa,+ kukumba mibadwo ya makolo,+ mikangano+ ndi kulimbana pa za Chilamulo,+ chifukwa zimenezi n’zosapindulitsa ndiponso n’zachabechabe.