Oweruza 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Motero Yehova anawapereka m’manja mwa Amidiyani+ kwa zaka 7. 2 Mbiri 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa+ za mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+
6 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Motero Yehova anawapereka m’manja mwa Amidiyani+ kwa zaka 7.
2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa+ za mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+