Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+

  • Rute 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho Naomi anati: “Taona m’bale wako wamasiye wabwerera kwa anthu a kwawo ndi kwa milungu yake.+ Bwerera naye limodzi.”+

  • 2 Mafumu 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Malo okwezeka amene anali kutsogolo+ kwa Yerusalemu kudzanja lamanja* la Phiri Lachiwonongeko,* amene Solomo+ mfumu ya Isiraeli inamangira Asitoreti+ chonyansa cha Asidoni, Kemosi+ chonyansa cha Mowabu, ndi Milikomu+ chonyansa cha ana a Amoni, mfumuyo inawasandutsa osayenera kulambirako.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena