Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Samalani, kuopera kuti mungachite pangano ndi anthu okhala m’dzikomo, pakuti iwo adzachita chiwerewere ndi milungu yawo+ ndi kupereka nsembe kwa milungu yawo.+ Chifukwa mukachita nawo pangano, mosakayikira wina adzakuitanani kunyumba kwake ndipo nanunso mudzadya nsembe yakeyo.+

  • 1 Mafumu 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Akaziwa anali ochokera m’mitundu imene Yehova anauza ana a Isiraeli kuti: “Musamapite pakati pawo+ ndipo iwonso asamabwere pakati panu, chifukwa ndithu adzapotoza mitima yanu kuti itsatire milungu yawo.”+ Amenewa ndi amene Solomo anaumirira+ kuwakonda.

  • Machitidwe 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”

  • 1 Akorinto 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ayi, koma ndikunena kuti zinthu zimene mitundu ina imapereka nsembe imazipereka kwa ziwanda,+ osati kwa Mulungu, ndipo sindikufuna kuti mukhale ogawana ndi ziwanda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena