Numeri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+ 1 Akorinto 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ayi, koma ndikunena kuti zinthu zimene mitundu ina imapereka nsembe imazipereka kwa ziwanda,+ osati kwa Mulungu, ndipo sindikufuna kuti mukhale ogawana ndi ziwanda.+
2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+
20 Ayi, koma ndikunena kuti zinthu zimene mitundu ina imapereka nsembe imazipereka kwa ziwanda,+ osati kwa Mulungu, ndipo sindikufuna kuti mukhale ogawana ndi ziwanda.+