Deuteronomo 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anali kupereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sanaidziwe,+Milungu yatsopano yongobwera kumene,+Imene makolo anu akale sanaidziwe. Salimo 106:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anali kupereka nsembe ana awo aamuna+Ndi ana awo aakazi kwa ziwanda.+
17 Iwo anali kupereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sanaidziwe,+Milungu yatsopano yongobwera kumene,+Imene makolo anu akale sanaidziwe.