Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 106:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo anayamba kulambira Baala wa ku Peori,+

      Ndi kudya nsembe zoperekedwa ku zinthu zakufa.+

  • Ezekieli 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 ngati sadya+ zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano m’mapiri,+ ngati sakweza maso ake kuyang’ana mafano onyansa a nyumba ya Isiraeli,+ ngati saipitsa mkazi wa mnzake,+ ngati sayandikira mkazi amene wadetsedwa,+

  • 2 Akorinto 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+

  • Chivumbulutso 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Komabe, ndakupeza ndi mlandu uwu. Walekerera mayi uja Yezebeli,+ amene amadzitcha mneneri. Iye amaphunzitsa+ ndi kusocheretsa akapolo anga+ kuti azichita dama+ ndi kudya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena