Salimo 115:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Manja ali nawo, koma sakhudza kanthu.+Mapazi ali nawo koma sayenda.+Satulutsa mawu ndi mmero wawo.+ Chivumbulutso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+
7 Manja ali nawo, koma sakhudza kanthu.+Mapazi ali nawo koma sayenda.+Satulutsa mawu ndi mmero wawo.+
14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+