1 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku lotsatira Aasidodi anadzuka m’mawa kwambiri, ndipo anapeza Dagoni atagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni ndi kumubwezeretsa pamalo ake.+ Yesaya 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
3 Tsiku lotsatira Aasidodi anadzuka m’mawa kwambiri, ndipo anapeza Dagoni atagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni ndi kumubwezeretsa pamalo ake.+
7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+