Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+

  • 1 Mbiri 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+

      Koma Yehova, ndiye anapanga kumwamba.+

  • Salimo 95:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu,+

      Ndiponso ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+

  • Salimo 96:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+

      Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+

  • Salimo 97:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+

      Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+

      Muweramireni, inu milungu yonse.+

  • Yesaya 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga+ ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera chifukwa chomuopa+ ndipo mitima ya Aiguputo idzasungunuka mkati mwa dzikolo.+

  • Zefaniya 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova adzawachititsa mantha,+ pakuti adzawondetsa milungu yonse ya padziko lapansi.+ Pamenepo anthu adzamugwadira,+ aliyense pamalo pake, zilumba zonse za mitundu ya anthu zidzamugwadira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena