1 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku lotsatira anthu a ku Asidodi atadzuka mʼmawa, anapeza Dagoni atagwa chafufumimba patsogolo pa Likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni nʼkumubwezeretsa pamalo ake.+
3 Tsiku lotsatira anthu a ku Asidodi atadzuka mʼmawa, anapeza Dagoni atagwa chafufumimba patsogolo pa Likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni nʼkumubwezeretsa pamalo ake.+