1 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku lotsatira Aasidodi anadzuka m’mawa kwambiri, ndipo anapeza Dagoni atagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni ndi kumubwezeretsa pamalo ake.+ Danieli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nebukadinezara anapanga fano lagolide.+ Fanoli linali lalitali mikono* 60 ndipo m’lifupi mwake linali mikono 6. Analiimika m’chigwa cha Dura, m’chigawo cha Babulo.+
3 Tsiku lotsatira Aasidodi anadzuka m’mawa kwambiri, ndipo anapeza Dagoni atagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni ndi kumubwezeretsa pamalo ake.+
3 Nebukadinezara anapanga fano lagolide.+ Fanoli linali lalitali mikono* 60 ndipo m’lifupi mwake linali mikono 6. Analiimika m’chigwa cha Dura, m’chigawo cha Babulo.+