1 Akorinto 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi. Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+
11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi.
4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+