-
Zekariya 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pa tsiku limenelo mapazi ake adzaponda paphiri la mitengo ya maolivi. Phiri limeneli lili moyang’anizana ndi Yerusalemu kumbali ya kum’mawa.+ Phiri la mitengo ya maolivi+ limeneli lidzagawanika pakati+ kuyambira kum’mawa mpaka kumadzulo. Zikadzatero, pakati pa mapiriwo padzakhala chigwa chachikulu kwambiri. Hafu imodzi ya phirilo idzasunthira kumpoto ndipo hafu inayo idzasunthira kum’mwera.
-