Ezekieli 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako, ulemerero wa Yehova+ unakwera m’mwamba kuchoka pakati pa mzindawo, n’kukaima pamwamba pa phiri+ limene lili kum’mawa kwa mzindawo.+ Machitidwe 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo anabwerera+ ku Yerusalemu, kuchokera kuphiri lotchedwa phiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*+
23 Kenako, ulemerero wa Yehova+ unakwera m’mwamba kuchoka pakati pa mzindawo, n’kukaima pamwamba pa phiri+ limene lili kum’mawa kwa mzindawo.+
12 Pamenepo anabwerera+ ku Yerusalemu, kuchokera kuphiri lotchedwa phiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*+