Ezekieli 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko ndinaona ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumbali ya kum’mawa.+ Mawu ake anali kumveka ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndipo dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+
2 Kumeneko ndinaona ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumbali ya kum’mawa.+ Mawu ake anali kumveka ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndipo dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+