Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kumeneko ndinaonako ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli,+ wofanana ndi zimene ndinaona kuchigwa zija.

  • Ezekieli 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli+ unachoka pamwamba pa akerubi+ pamene unali, ndipo unapita pakhomo la malo opatulika.+ Kenako Mulungu anayamba kulankhula mofuula kwa munthu wovala zovala zansalu uja,+ yemwe m’chiuno mwake munali kachikwama ka mlembi konyamuliramo inki ndi zolembera.

  • Ezekieli 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi n’kupita pakhomo la nyumba yopatulika, ndipo mtambo+ unadzaza nyumbayo pang’onopang’ono. Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza m’bwalo lonse la nyumbayo.

  • Ezekieli 43:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno ulemerero+ wa Yehova unalowa m’Nyumbayo kudzera pachipata choyang’ana kum’mawa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena