Ezekieli 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero ndinanyamuka n’kupita kuchigwako. Kumeneko ndinangoona kuti ulemerero wa Yehova waimirira,+ ngati ulemerero umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+ Ezekieli 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kumeneko ndinaonako ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli,+ wofanana ndi zimene ndinaona kuchigwa zija. Ezekieli 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano akerubi+ aja anatambasula mapiko awo ndipo mawilo anali pambali pawo.+ Ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli unali pamwamba pa mitu yawo.+
23 Chotero ndinanyamuka n’kupita kuchigwako. Kumeneko ndinangoona kuti ulemerero wa Yehova waimirira,+ ngati ulemerero umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+
22 Tsopano akerubi+ aja anatambasula mapiko awo ndipo mawilo anali pambali pawo.+ Ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli unali pamwamba pa mitu yawo.+