Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 40:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+

  • 1 Mafumu 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ansembe atatuluka m’malo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.

  • 2 Mbiri 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano anthu oimba malipenga ndi oimba pakamwa anayamba kuimba mogwirizana+ n’kumamveka ngati mawu amodzi otamanda ndi kuthokoza Yehova. Komanso anayamba kuimba+ ndi malipenga, zinganga, ndi zoimbira zina potamanda+ Yehova ndi mawu akuti, “chifukwa iye ndi wabwino,+ pakuti kukoma mtima kwake kosatha+ kudzakhala mpaka kalekale.” Kenako mtambo unadzaza nyumbayo,+ nyumba ya Yehova.+

  • Ezekieli 43:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako mzimu unandidzutsa+ m’kupita nane kubwalo lamkati. Kumeneko ndinangoona kuti ulemerero wa Yehova wadzaza m’Nyumba ija.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena