1 Mbiri 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yamikani Yehova anthu inu, chifukwa iye ndi wabwino,+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ 2 Mbiri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino+ zimene Yehova anachitira Davide, Solomo, ndiponso zimene anachitira anthu ake Aisiraeli.+
34 Yamikani Yehova anthu inu, chifukwa iye ndi wabwino,+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino+ zimene Yehova anachitira Davide, Solomo, ndiponso zimene anachitira anthu ake Aisiraeli.+