2 Mbiri 6:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano inu Yehova Mulungu nyamukani+ mulowe mu mpumulo wanu,+ inuyo ndi Likasa limene mumasonyezera mphamvu zanu.+ Ansembe anu, inu Yehova Mulungu, avale chipulumutso ndipo okhulupirika anu asangalale chifukwa cha zabwino.+
41 Tsopano inu Yehova Mulungu nyamukani+ mulowe mu mpumulo wanu,+ inuyo ndi Likasa limene mumasonyezera mphamvu zanu.+ Ansembe anu, inu Yehova Mulungu, avale chipulumutso ndipo okhulupirika anu asangalale chifukwa cha zabwino.+