Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 40:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho.

  • 1 Mafumu 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ansembe atatuluka m’malo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.

  • 2 Mbiri 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona.

  • Yesaya 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.”

  • Ezekieli 44:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena