1 Mafumu 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ansembe atatuluka mʼmalo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.+