1 Mafumu 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ansembe atatuluka m’malo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.