Amosi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa.
12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa.