Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 33:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Adzaimbira anthu n’kunena kuti,

      ‘Ndachimwa,+ ndakhotetsa zimene zinali zowongoka,

      Ndipo sindinayenere kuchita zimenezi.

  • Miyambo 29:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+

  • Yesaya 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+

  • Mateyu 26:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni wonama kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha+

  • Machitidwe 7:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Inde, iwo anapha+ amene analengezeratu za kubwera kwa Wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndi kumupha,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena